R JAI – NENA (Official MP3 and Lyrics)

  2
  245

  LYRICS UPDATED BY JAY ODA ASE (The song has been mixed and mastered by Fadoum)

  INTRO

  Hello, how’re you doing?
  Papita masiku angapo, I can not hear from you
  Kodi phone ndizingoyimba, ine ndekhandekha?
  Kodi ndizingokuyendela, ine ndekhandekha?
  Mwina chomwe ufuna, ndicho phada basi
  Mwina sunamalize kunsakha the best one for you
  When I say I love you umangoti zikomo
  When I say I miss you yankho lako ndi tilipo

  HOOK

  Don’t test me
  Mwina chatha kale
  Don’t test me
  (Chatha?.•°×2 Tell me the truth)
  Don’t test me
  Usanditayitse nthawi
  Don’t test me
  Ungonena.•°×2

  VERSE 2

  Pa WhatsApp, mwandipanga hide
  Kuti tichezeko Kodi n’chite kupanga apply
  Nthawi yoti mundipatse ine,
  Mwapeleka kwa ma bestie mwati
  Chifukwa ndine wofatsa ine
  Mwatino munditole
  Mukhala ngati muli single (single)
  Mtima wanga si jingle (jingle)
  Sin’ngakhale MG 2, sindimadzikaikira No!!
  Ndibwino undiwuze than kunditayitsa nthawi
  Za banja sukambako, I’m I the one?
  Or you’re waiting for someone else?

     BACK TO THE HOOK

  VERSE 3

  Sindifuna n’sinthe
  Kuti ndiyambe uhule because of you
  Sindifuna nkhawa, just because someone is not loving me
  Ndisafele dzina kuti I got someone in my life
  Ndizafele zina not because of heartbreak
  Mukhala ngati muli single (single)
  Mtima wanga si jingle (jingle)
  Singakhale MG 2, sindimazikaikira No!!
  Ndibwino undiuze than kunditayitsa nthawi
  Za banja sukambako, I’m I the one?
  Or you’re waiting for someone else?

  IF YOU ARE IN MALAWI, SOUTH AFRICA, ZAMBIA OR TANZANIA, CONTACT JAY ODA ASE FOR MASSIVE PROMO +265888282196

  2 COMMENTS

  LEAVE A REPLY